Woyimba wazaka 74, Jetu, alandira plot kuchokera ku Eagles Real Estate Consultants

[Nyasa Times] - 8/05/2024

Kampani yogulitsa malo ya Eagles Real Estate Consultants yapeleka plot kwa oyimba Jetu yemwe dzina lake lenileni ndi Christina Kholiyo pomulimbikitsa pa ntchito yake yoyimba komanso kusangalatsa anthu. Mkulu owona za malonda ku kampaniyi a Roshan Thole wati plot-yi yomwe ili ku Lilongwe ku (...)


  e-mail